×

Ndipo tikam’patsa munthu zokoma zathu, iye amatembenuka ndi kuchita mwano ndipo amakhala 17:83 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:83) ayat 83 in Chichewa

17:83 Surah Al-Isra’ ayat 83 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 83 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَإِذَآ أَنۡعَمۡنَا عَلَى ٱلۡإِنسَٰنِ أَعۡرَضَ وَنَـَٔا بِجَانِبِهِۦ وَإِذَا مَسَّهُ ٱلشَّرُّ كَانَ يَـُٔوسٗا ﴾
[الإسرَاء: 83]

Ndipo tikam’patsa munthu zokoma zathu, iye amatembenuka ndi kuchita mwano ndipo amakhala kutali ndi njira yoyenera. Ndipo zikam’peza zoipa amakhala wotaya mtima kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا أنعمنا على الإنسان أعرض ونأى بجانبه وإذا مسه الشر كان يئوسا, باللغة نيانجا

﴿وإذا أنعمنا على الإنسان أعرض ونأى بجانبه وإذا مسه الشر كان يئوسا﴾ [الإسرَاء: 83]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tikampatsa chisomo munthu, (monga moyo wangwiro ndikupeza bwino), amatembenuka (ndikusiya kutikumbukira ndikutipempha), ndipo amadziika kutali (ndi Ife chifukwa chakudzitama ndikudzikuza), koma masautso akamkhudza, (monga matenda ndi umphawi) amataya mtima kwambiri
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek