×

Nena, “Munthu aliyense amachita molingana ndi chikhalidwe chake koma Ambuye wanu amadziwa 17:84 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:84) ayat 84 in Chichewa

17:84 Surah Al-Isra’ ayat 84 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 84 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿قُلۡ كُلّٞ يَعۡمَلُ عَلَىٰ شَاكِلَتِهِۦ فَرَبُّكُمۡ أَعۡلَمُ بِمَنۡ هُوَ أَهۡدَىٰ سَبِيلٗا ﴾
[الإسرَاء: 84]

Nena, “Munthu aliyense amachita molingana ndi chikhalidwe chake koma Ambuye wanu amadziwa yemwe watsogozedwa bwino panjira yachilungamo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل كل يعمل على شاكلته فربكم أعلم بمن هو أهدى سبيلا, باللغة نيانجا

﴿قل كل يعمل على شاكلته فربكم أعلم بمن هو أهدى سبيلا﴾ [الإسرَاء: 84]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena (iwe Mneneri, kwa osakhulupirira a Chikuraishi,): “Aliyense (wa ife ndi inu) akuchita ntchito (zake ndikuyenda panjira yake) ndipo Mbuye wanu Ngodziwa kwambiri za yemwe ali panjira yolondola (potsatira choonadi).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek