×

IwoakukufunsazaMzimu.Ndiponena,“Ambuyewanga ndiye amene adziwa za iwo. Ndipo inu simudapatsidwe nzeru koma pang’ono 17:85 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:85) ayat 85 in Chichewa

17:85 Surah Al-Isra’ ayat 85 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 85 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَيَسۡـَٔلُونَكَ عَنِ ٱلرُّوحِۖ قُلِ ٱلرُّوحُ مِنۡ أَمۡرِ رَبِّي وَمَآ أُوتِيتُم مِّنَ ٱلۡعِلۡمِ إِلَّا قَلِيلٗا ﴾
[الإسرَاء: 85]

IwoakukufunsazaMzimu.Ndiponena,“Ambuyewanga ndiye amene adziwa za iwo. Ndipo inu simudapatsidwe nzeru koma pang’ono pokha.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ويسألونك عن الروح قل الروح من أمر ربي وما أوتيتم من العلم, باللغة نيانجا

﴿ويسألونك عن الروح قل الروح من أمر ربي وما أوتيتم من العلم﴾ [الإسرَاء: 85]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akukufunsa (iwe, Muhammad (s.a.w), anthu ako mokhwiriziridwa ndi Ayuda) za Mzimu. Nena: “Mzimu ndi chinthu chomwe akuchidziwa Mbuye wanga Yekha; ndipo inu simudapatsidwe nzeru (zozindikilira zinthu) koma pang’ono chabe, (poyerekeza ndi nzeru za Allah).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek