×

Ndithudi talongosola kwa anthu mu Korani ino chitsanzo chilichonse. Komabe anthu ambiri 17:89 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:89) ayat 89 in Chichewa

17:89 Surah Al-Isra’ ayat 89 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 89 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَلَقَدۡ صَرَّفۡنَا لِلنَّاسِ فِي هَٰذَا ٱلۡقُرۡءَانِ مِن كُلِّ مَثَلٖ فَأَبَىٰٓ أَكۡثَرُ ٱلنَّاسِ إِلَّا كُفُورٗا ﴾
[الإسرَاء: 89]

Ndithudi talongosola kwa anthu mu Korani ino chitsanzo chilichonse. Komabe anthu ambiri akana choonadi ndi kukhala osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد صرفنا للناس في هذا القرآن من كل مثل فأبى أكثر الناس, باللغة نيانجا

﴿ولقد صرفنا للناس في هذا القرآن من كل مثل فأبى أكثر الناس﴾ [الإسرَاء: 89]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu tawalongosolera anthu, m’Qur’an iyi; mkulongosola kwa njira zosiyanasiyana ndikupereka fanizo lamtundu uliwonse. Ndipo anthu ambiri akukana (zonsezo) koma kusakhulupirira basi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek