Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 88 - الإسرَاء - Page - Juz 15
﴿قُل لَّئِنِ ٱجۡتَمَعَتِ ٱلۡإِنسُ وَٱلۡجِنُّ عَلَىٰٓ أَن يَأۡتُواْ بِمِثۡلِ هَٰذَا ٱلۡقُرۡءَانِ لَا يَأۡتُونَ بِمِثۡلِهِۦ وَلَوۡ كَانَ بَعۡضُهُمۡ لِبَعۡضٖ ظَهِيرٗا ﴾
[الإسرَاء: 88]
﴿قل لئن اجتمعت الإنس والجن على أن يأتوا بمثل هذا القرآن لا﴾ [الإسرَاء: 88]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Ngakhale atasonkhana anthu ndi ziwanda (mothandizana) kuti abwere ndi buku longa ili la Qur’an (mukayalidwe ka mawu ndi matanthauzo ake), sangathe kubweretsa longa ilo, ngakhale atathandizana wina ndi mnzake.” |