×

Opanda kuonjezera mawu oti, “Ngati Mulungu afuna.” Ndipo kumbukira Ambuye wako ngati 18:24 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:24) ayat 24 in Chichewa

18:24 Surah Al-Kahf ayat 24 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 24 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿إِلَّآ أَن يَشَآءَ ٱللَّهُۚ وَٱذۡكُر رَّبَّكَ إِذَا نَسِيتَ وَقُلۡ عَسَىٰٓ أَن يَهۡدِيَنِ رَبِّي لِأَقۡرَبَ مِنۡ هَٰذَا رَشَدٗا ﴾
[الكَهف: 24]

Opanda kuonjezera mawu oti, “Ngati Mulungu afuna.” Ndipo kumbukira Ambuye wako ngati uiwala ndipo unene kuti, “Ngati ndikotheka Mulungu anditsogolere ine ndi kundibweretsa kufupi ndi choonadi m’malo mwa ichi.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إلا أن يشاء الله واذكر ربك إذا نسيت وقل عسى أن يهدين, باللغة نيانجا

﴿إلا أن يشاء الله واذكر ربك إذا نسيت وقل عسى أن يهدين﴾ [الكَهف: 24]

Khaled Ibrahim Betala
““Koma (utsogoze liwu lakuti): Insha Allah, (Allah akafuna!)” Ndipo mukumbuke Mbuye wako ukaiwala ponena kuti: “Mwina Mbuye wanga anditsogolera pa njira yapafupi pachiongoko kuposa iyi.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek