Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 44 - الكَهف - Page - Juz 15
﴿هُنَالِكَ ٱلۡوَلَٰيَةُ لِلَّهِ ٱلۡحَقِّۚ هُوَ خَيۡرٞ ثَوَابٗا وَخَيۡرٌ عُقۡبٗا ﴾
[الكَهف: 44]
﴿هنالك الولاية لله الحق هو خير ثوابا وخير عقبا﴾ [الكَهف: 44]
| Khaled Ibrahim Betala “Pamalo potere chitetezo chimakhala cha Allah Yekha Woona. Iye Ngolipira bwino, ndiponso Wabwino (pakudza) ndi malekezero abwino |