Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 5 - الكَهف - Page - Juz 15
﴿مَّا لَهُم بِهِۦ مِنۡ عِلۡمٖ وَلَا لِأٓبَآئِهِمۡۚ كَبُرَتۡ كَلِمَةٗ تَخۡرُجُ مِنۡ أَفۡوَٰهِهِمۡۚ إِن يَقُولُونَ إِلَّا كَذِبٗا ﴾
[الكَهف: 5]
﴿ما لهم به من علم ولا لآبائهم كبرت كلمة تخرج من أفواههم﴾ [الكَهف: 5]
Khaled Ibrahim Betala “Iwo pabodza lawolo alibe kuzindikira chinthu chilichonse chanzeru ngakhale makolo awo. Lakula kwabasi liwu lomwe likutuluka mkamwa mwawo. Sanena china koma bodza basi |