×

Pamene Ife tidawauza angelo kuti, “Mugwadireni Adamu.” Motero onse anamugwadira Iye kupatula 18:50 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:50) ayat 50 in Chichewa

18:50 Surah Al-Kahf ayat 50 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 50 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿وَإِذۡ قُلۡنَا لِلۡمَلَٰٓئِكَةِ ٱسۡجُدُواْ لِأٓدَمَ فَسَجَدُوٓاْ إِلَّآ إِبۡلِيسَ كَانَ مِنَ ٱلۡجِنِّ فَفَسَقَ عَنۡ أَمۡرِ رَبِّهِۦٓۗ أَفَتَتَّخِذُونَهُۥ وَذُرِّيَّتَهُۥٓ أَوۡلِيَآءَ مِن دُونِي وَهُمۡ لَكُمۡ عَدُوُّۢۚ بِئۡسَ لِلظَّٰلِمِينَ بَدَلٗا ﴾
[الكَهف: 50]

Pamene Ife tidawauza angelo kuti, “Mugwadireni Adamu.” Motero onse anamugwadira Iye kupatula Satana amene adali mmodzi wa ziwanda ndipo adanyoza lamulo la Ambuye wake. Kodi mudzasankha iyeyo pamodzi ndi ana ake kukhala okutetezani ndi kukuthandizani m’malo mwa Ine, pamene iwo ndi adani? Kodi ndi choipa chotani chimene anthu ochita zoipa asankha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذ قلنا للملائكة اسجدوا لآدم فسجدوا إلا إبليس كان من الجن ففسق, باللغة نيانجا

﴿وإذ قلنا للملائكة اسجدوا لآدم فسجدوا إلا إبليس كان من الجن ففسق﴾ [الكَهف: 50]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (kumbuka) pamene tidawauza angelo: “Mchitireni sijida Adam (mugwadireni momulemekeza).” Onse adachitadi sijida kupatula Iblis. Iye adali mmodzi wa ziwanda, ndipo adatuluka m’chilamulo cha Mbuye wake. Kodi iye ndi mbumba yake mukuwalola kukhala abwenzi (anu) kusiya Ine, pomwe iwo ndiadani anu? Taonani kuipa kusintha kwa anthu oipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek