×

Ine sindidawaonetse kalengedwe ka kumwamba ndi dziko lapansi kapena kalengedwe kawo komwe 18:51 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:51) ayat 51 in Chichewa

18:51 Surah Al-Kahf ayat 51 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 51 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿۞ مَّآ أَشۡهَدتُّهُمۡ خَلۡقَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ وَلَا خَلۡقَ أَنفُسِهِمۡ وَمَا كُنتُ مُتَّخِذَ ٱلۡمُضِلِّينَ عَضُدٗا ﴾
[الكَهف: 51]

Ine sindidawaonetse kalengedwe ka kumwamba ndi dziko lapansi kapena kalengedwe kawo komwe ndiponso Ine sindidawasankhe, osocheretsa anthu, kukhala ondithandiza anga

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ما أشهدتهم خلق السموات والأرض ولا خلق أنفسهم وما كنت متخذ المضلين, باللغة نيانجا

﴿ما أشهدتهم خلق السموات والأرض ولا خلق أنفسهم وما كنت متخذ المضلين﴾ [الكَهف: 51]

Khaled Ibrahim Betala
“Sindidawachite (iwo) kukhala mboni nkulenga kwa thambo ndi nthaka, ngakhale kuwalenga kwawo ndipo sindidawalole osokeretsa kukhala athandizi (Anga)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek