Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 98 - الكَهف - Page - Juz 16
﴿قَالَ هَٰذَا رَحۡمَةٞ مِّن رَّبِّيۖ فَإِذَا جَآءَ وَعۡدُ رَبِّي جَعَلَهُۥ دَكَّآءَۖ وَكَانَ وَعۡدُ رَبِّي حَقّٗا ﴾
[الكَهف: 98]
﴿قال هذا رحمة من ربي فإذا جاء وعد ربي جعله دكاء وكان﴾ [الكَهف: 98]
Khaled Ibrahim Betala “(Iye) adati: “Ichi ndi chifundo chochokera kwa Mbuye wanga; koma likadzafika lonjezo la Mbuye wanga (kudza kwa Qiyâma), adzachiswanyaswanya; ndipo lonjezo la Mbuye wanga nloona.” |