×

Sizili zoyenera kuti Mulungu akhale ndi mwana wamwamuna! Iye ayeretsedwe ku zimenezo. 19:35 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Maryam ⮕ (19:35) ayat 35 in Chichewa

19:35 Surah Maryam ayat 35 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 35 - مَريَم - Page - Juz 16

﴿مَا كَانَ لِلَّهِ أَن يَتَّخِذَ مِن وَلَدٖۖ سُبۡحَٰنَهُۥٓۚ إِذَا قَضَىٰٓ أَمۡرٗا فَإِنَّمَا يَقُولُ لَهُۥ كُن فَيَكُونُ ﴾
[مَريَم: 35]

Sizili zoyenera kuti Mulungu akhale ndi mwana wamwamuna! Iye ayeretsedwe ku zimenezo. Ngati Iye afuna chinthu, Iye amangonena kuti, “Chikhale” ndipo chimakhaladi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ما كان لله أن يتخذ من ولد سبحانه إذا قضى أمرا فإنما, باللغة نيانجا

﴿ما كان لله أن يتخذ من ولد سبحانه إذا قضى أمرا فإنما﴾ [مَريَم: 35]

Khaled Ibrahim Betala
“Sikoyenera kwa Allah kudzipangira mwana. Iye (Allah) wapatukana ndi zimenezi. Akafuna chinthu, amangonena kwa chinthucho: “Chitika,” ndipo icho chimachitikadi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek