Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 36 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿وَإِنَّ ٱللَّهَ رَبِّي وَرَبُّكُمۡ فَٱعۡبُدُوهُۚ هَٰذَا صِرَٰطٞ مُّسۡتَقِيمٞ ﴾
[مَريَم: 36]
﴿وإن الله ربي وربكم فاعبدوه هذا صراط مستقيم﴾ [مَريَم: 36]
Khaled Ibrahim Betala “(Isa (Yesu) adati:) “Ndipo ndithu Allah ndi Mbuye wanga ndiponso Mbuye wanu. Choncho mpembedzeni; iyi ndinjira yolunjika (yokufikitsani ku mtendere) |