×

Kodi iwo adzaona ndi kumva momveka bwanji pa tsiku limene adzaonekera pa 19:38 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Maryam ⮕ (19:38) ayat 38 in Chichewa

19:38 Surah Maryam ayat 38 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 38 - مَريَم - Page - Juz 16

﴿أَسۡمِعۡ بِهِمۡ وَأَبۡصِرۡ يَوۡمَ يَأۡتُونَنَا لَٰكِنِ ٱلظَّٰلِمُونَ ٱلۡيَوۡمَ فِي ضَلَٰلٖ مُّبِينٖ ﴾
[مَريَم: 38]

Kodi iwo adzaona ndi kumva momveka bwanji pa tsiku limene adzaonekera pa maso pathu! Koma anthu ochita zoipa lero ali mu chisokonezo choonekeratu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أسمع بهم وأبصر يوم يأتوننا لكن الظالمون اليوم في ضلال مبين, باللغة نيانجا

﴿أسمع بهم وأبصر يوم يأتوننا لكن الظالمون اليوم في ضلال مبين﴾ [مَريَم: 38]

Khaled Ibrahim Betala
“Taona kumvetsetsa kwawo ndi kupenyetsetsa kwawo tsiku lodzatidzera, (kudzanenedwa kuti:) “Koma osalungama lero ali m’kusokera koonekera.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek