×

Motero pali Ambuye wako; ndithudi Tidzawasonkhanitsa pamodzi ndi a Satana ndipo onse 19:68 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Maryam ⮕ (19:68) ayat 68 in Chichewa

19:68 Surah Maryam ayat 68 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 68 - مَريَم - Page - Juz 16

﴿فَوَرَبِّكَ لَنَحۡشُرَنَّهُمۡ وَٱلشَّيَٰطِينَ ثُمَّ لَنُحۡضِرَنَّهُمۡ حَوۡلَ جَهَنَّمَ جِثِيّٗا ﴾
[مَريَم: 68]

Motero pali Ambuye wako; ndithudi Tidzawasonkhanitsa pamodzi ndi a Satana ndipo onse tidzawabweretsa m’mphepete mwa Gahena atagwada

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فوربك لنحشرنهم والشياطين ثم لنحضرنهم حول جهنم جثيا, باللغة نيانجا

﴿فوربك لنحشرنهم والشياطين ثم لنحضرنهم حول جهنم جثيا﴾ [مَريَم: 68]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho ndikulumbira Mbuye wako, ndithu tidzawasonkhanitsa iwo pamodzi ndi asatana; ndipo tidzawafikitsa m’mphepete mwa Jahannam uku atagwada
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek