×

Anthu ambiri otsatira a m’Buku amafuna kuti akusokeretse chifukwa cha kaduka kuti 2:109 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:109) ayat 109 in Chichewa

2:109 Surah Al-Baqarah ayat 109 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 109 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَدَّ كَثِيرٞ مِّنۡ أَهۡلِ ٱلۡكِتَٰبِ لَوۡ يَرُدُّونَكُم مِّنۢ بَعۡدِ إِيمَٰنِكُمۡ كُفَّارًا حَسَدٗا مِّنۡ عِندِ أَنفُسِهِم مِّنۢ بَعۡدِ مَا تَبَيَّنَ لَهُمُ ٱلۡحَقُّۖ فَٱعۡفُواْ وَٱصۡفَحُواْ حَتَّىٰ يَأۡتِيَ ٱللَّهُ بِأَمۡرِهِۦٓۗ إِنَّ ٱللَّهَ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٞ ﴾
[البَقَرَة: 109]

Anthu ambiri otsatira a m’Buku amafuna kuti akusokeretse chifukwa cha kaduka kuti ukhale osakhulupirira ngakhale pamene choonadi chaonekera poyera kwa iwo. Koma akhululukire mpaka pamene Mulungu abweretsa lamulo lake. Ndithudi Mulungu ali ndi mphamvu pa zinthu zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ود كثير من أهل الكتاب لو يردونكم من بعد إيمانكم كفارا حسدا, باللغة نيانجا

﴿ود كثير من أهل الكتاب لو يردونكم من بعد إيمانكم كفارا حسدا﴾ [البَقَرَة: 109]

Khaled Ibrahim Betala
“Ambiri mwa amene anapatsidwa mabuku, akufuna kukubwezani (kukutembenuzani) kuti mukhale osakhulupirira pambuyo pa chikhulupiliro chanu, chifukwa chadumbo lomwe lili m’mitima mwawo (lomwe lawapeza) pambuyo powaonekera choonadi poyera. Choncho akhululukireni ndi kuwasiya kufikira Allah adzabweretse lamulo Lake*; ndithudi Allah Ngokhoza chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek