×

Ndipo pitiriza mapemphero ndipo pereka msonkho wothandiza anthu osauka. Ndipo chilichonse chabwino 2:110 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:110) ayat 110 in Chichewa

2:110 Surah Al-Baqarah ayat 110 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 110 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَأَقِيمُواْ ٱلصَّلَوٰةَ وَءَاتُواْ ٱلزَّكَوٰةَۚ وَمَا تُقَدِّمُواْ لِأَنفُسِكُم مِّنۡ خَيۡرٖ تَجِدُوهُ عِندَ ٱللَّهِۗ إِنَّ ٱللَّهَ بِمَا تَعۡمَلُونَ بَصِيرٞ ﴾
[البَقَرَة: 110]

Ndipo pitiriza mapemphero ndipo pereka msonkho wothandiza anthu osauka. Ndipo chilichonse chabwino chimene mungatsogoze mudzachipeza kwa Mulungu. Ndithudi Mulungu amaona zonse zimene muli kuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأقيموا الصلاة وآتوا الزكاة وما تقدموا لأنفسكم من خير تجدوه عند الله, باللغة نيانجا

﴿وأقيموا الصلاة وآتوا الزكاة وما تقدموا لأنفسكم من خير تجدوه عند الله﴾ [البَقَرَة: 110]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pempherani Swala moyenera ndiponso perekani Zakaat. Ndipo chilichonse chabwino chimene mukudzitsogozera mukachipeza kwa Allah. Ndithudi, Allah akuona zonse zimene mukuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek