×

Iwo amanena kuti: “Palibe amene adzalowa ku Paradiso kupatula yekhayo amene ali 2:111 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:111) ayat 111 in Chichewa

2:111 Surah Al-Baqarah ayat 111 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 111 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَقَالُواْ لَن يَدۡخُلَ ٱلۡجَنَّةَ إِلَّا مَن كَانَ هُودًا أَوۡ نَصَٰرَىٰۗ تِلۡكَ أَمَانِيُّهُمۡۗ قُلۡ هَاتُواْ بُرۡهَٰنَكُمۡ إِن كُنتُمۡ صَٰدِقِينَ ﴾
[البَقَرَة: 111]

Iwo amanena kuti: “Palibe amene adzalowa ku Paradiso kupatula yekhayo amene ali Myuda kapena Mkhirisitu. Zimenezo ndizo zilako lako zawo. Nena: “Bweretsani umboni wanu ngati muli ndi chilungamo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقالوا لن يدخل الجنة إلا من كان هودا أو نصارى تلك أمانيهم, باللغة نيانجا

﴿وقالوا لن يدخل الجنة إلا من كان هودا أو نصارى تلك أمانيهم﴾ [البَقَرَة: 111]

Khaled Ibrahim Betala
“Eti akunena: “Palibe amene adzalowe ku Munda wamtendere koma amene ali Myuda Kapena Mkhirisitu.” Zimenezo nzokhumba zawo chabe. Nena: “Bweretsani umboni wanu ngati mukunena zoona.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek