×

Ayuda anati: Akhirisitu satsatira china chilichonse chabwino pamene Akhirisitu anati, Ayuda satsatira 2:113 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:113) ayat 113 in Chichewa

2:113 Surah Al-Baqarah ayat 113 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 113 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَقَالَتِ ٱلۡيَهُودُ لَيۡسَتِ ٱلنَّصَٰرَىٰ عَلَىٰ شَيۡءٖ وَقَالَتِ ٱلنَّصَٰرَىٰ لَيۡسَتِ ٱلۡيَهُودُ عَلَىٰ شَيۡءٖ وَهُمۡ يَتۡلُونَ ٱلۡكِتَٰبَۗ كَذَٰلِكَ قَالَ ٱلَّذِينَ لَا يَعۡلَمُونَ مِثۡلَ قَوۡلِهِمۡۚ فَٱللَّهُ يَحۡكُمُ بَيۡنَهُمۡ يَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِ فِيمَا كَانُواْ فِيهِ يَخۡتَلِفُونَ ﴾
[البَقَرَة: 113]

Ayuda anati: Akhirisitu satsatira china chilichonse chabwino pamene Akhirisitu anati, Ayuda satsatira chilichonse ngakhale kuti onse amawerenga Buku la Mulungu. Izi zili chimodzimodzi ndi zimene anthu osazindikira amalankhula. Mulungu adzaweruza pakati pawo tsiku la chiweruzo mu zimene adali kusiyana maganizo awo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقالت اليهود ليست النصارى على شيء وقالت النصارى ليست اليهود على شيء, باللغة نيانجا

﴿وقالت اليهود ليست النصارى على شيء وقالت النصارى ليست اليهود على شيء﴾ [البَقَرَة: 113]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo Ayuda akumanena: “Akhrisitu alibe chilichonse (chotsamira pa chipembedzo chawo);” naonso Akhrisitu akumanena: “Ayuda alibe chilichonse (chotsamira pa chipembedzo chawo),” pomwe onsewa akuwerenga buku (lomwe adawavumbulutsira popanda kutsatira zili m’bukulo). Momwemonso akunena amene sali odziwa (Arabu opembedza mafano) monga zonena zawo (Ayuda). Allah adzaweruza pakati pawo tsiku la chimaliziro pa zomwe adali kusiyana
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek