×

Ndithudi Ife takutumiza ndi choonadi kuti ulalikire uthenga wosangalatsa ndi kupereka chenjezo. 2:119 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:119) ayat 119 in Chichewa

2:119 Surah Al-Baqarah ayat 119 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 119 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿إِنَّآ أَرۡسَلۡنَٰكَ بِٱلۡحَقِّ بَشِيرٗا وَنَذِيرٗاۖ وَلَا تُسۡـَٔلُ عَنۡ أَصۡحَٰبِ ٱلۡجَحِيمِ ﴾
[البَقَرَة: 119]

Ndithudi Ife takutumiza ndi choonadi kuti ulalikire uthenga wosangalatsa ndi kupereka chenjezo. Siudzafunsidwa za anthu okhala ku moto

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إنا أرسلناك بالحق بشيرا ونذيرا ولا تسأل عن أصحاب الجحيم, باللغة نيانجا

﴿إنا أرسلناك بالحق بشيرا ونذيرا ولا تسأل عن أصحاب الجحيم﴾ [البَقَرَة: 119]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, Ife takutumiza (iwe Mtumiki {s.a.w}) ndi choonadi kuti ukhale wouza nkhani zabwino ndi wochenjeza. Ndipo siudzafunsidwa za anthu a ku Moto
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek