×

Ndipo anthu osadziwa amati: “Kodi ndi chifukwa chiyani Mulungu sakutilankhula kapena kutibweretsera 2:118 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:118) ayat 118 in Chichewa

2:118 Surah Al-Baqarah ayat 118 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 118 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَقَالَ ٱلَّذِينَ لَا يَعۡلَمُونَ لَوۡلَا يُكَلِّمُنَا ٱللَّهُ أَوۡ تَأۡتِينَآ ءَايَةٞۗ كَذَٰلِكَ قَالَ ٱلَّذِينَ مِن قَبۡلِهِم مِّثۡلَ قَوۡلِهِمۡۘ تَشَٰبَهَتۡ قُلُوبُهُمۡۗ قَدۡ بَيَّنَّا ٱلۡأٓيَٰتِ لِقَوۡمٖ يُوقِنُونَ ﴾
[البَقَرَة: 118]

Ndipo anthu osadziwa amati: “Kodi ndi chifukwa chiyani Mulungu sakutilankhula kapena kutibweretsera chizindikiro?” Mmenemo ndi mmene adanenera anthu amene adalipo kale iwo asadadze. Mitima yawo yonse ndi yolingana. Ndithudi Ife tafotokoza zizindikiro kwa anthu okhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال الذين لا يعلمون لولا يكلمنا الله أو تأتينا آية كذلك قال, باللغة نيانجا

﴿وقال الذين لا يعلمون لولا يكلمنا الله أو تأتينا آية كذلك قال﴾ [البَقَرَة: 118]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo aja osadziwa akunena: “Bwanji Allah sakutiyankhula ife? Kapena kutibwerera chizindikiro (chizizwa)?” Mofanana ndi zoyankhula zawozo adanenanso amene adalipo kale. Mitima yawo yalingana. Ndithu Ife tazifotokoza zizindikiro momveka kwa anthu otsimikiza (m’chikhulupiliro)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek