Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 162 - البَقَرَة - Page - Juz 2
﴿خَٰلِدِينَ فِيهَا لَا يُخَفَّفُ عَنۡهُمُ ٱلۡعَذَابُ وَلَا هُمۡ يُنظَرُونَ ﴾
[البَقَرَة: 162]
﴿خالدين فيها لا يخفف عنهم العذاب ولا هم ينظرون﴾ [البَقَرَة: 162]
Khaled Ibrahim Betala “M’menemo (m’chilango cha matembelero) adzakhalamo nthawi yaitali. Ndipo chilango sichidzapeputsidwa kwa iwo, ndipo sadzapatsidwa nthawi (yopumula) |