×

Iwo ali ngati munthu amene adasonkha moto ndipo pamene moto unali nkuyaka, 2:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:17) ayat 17 in Chichewa

2:17 Surah Al-Baqarah ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 17 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿مَثَلُهُمۡ كَمَثَلِ ٱلَّذِي ٱسۡتَوۡقَدَ نَارٗا فَلَمَّآ أَضَآءَتۡ مَا حَوۡلَهُۥ ذَهَبَ ٱللَّهُ بِنُورِهِمۡ وَتَرَكَهُمۡ فِي ظُلُمَٰتٖ لَّا يُبۡصِرُونَ ﴾
[البَقَرَة: 17]

Iwo ali ngati munthu amene adasonkha moto ndipo pamene moto unali nkuyaka, kuunika zimene zili m’mbali mwake, Mulungu anachotsa kuwala kwawo ndipo adawasiya ali mu mdima waukulu wosathanso kuona

❮ Previous Next ❯

ترجمة: مثلهم كمثل الذي استوقد نارا فلما أضاءت ما حوله ذهب الله بنورهم, باللغة نيانجا

﴿مثلهم كمثل الذي استوقد نارا فلما أضاءت ما حوله ذهب الله بنورهم﴾ [البَقَرَة: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Fanizo lawo lili ngati (munthu wa paulendo wafungatiridwa ndi mdima) yemwe wayatsa moto; ndipo pamene udaunika zomwe zidali m’mphepete mwake, Allah nkuwachotsera kuunika kwawoko nawasiya mu mdima osatha kuona
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek