×

Ndipo pamene zimanenedwa kwa iwo kuti: Tsatirani zimene Mulungu wavumbulutsa, iwo amayankha: 2:170 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:170) ayat 170 in Chichewa

2:170 Surah Al-Baqarah ayat 170 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 170 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿وَإِذَا قِيلَ لَهُمُ ٱتَّبِعُواْ مَآ أَنزَلَ ٱللَّهُ قَالُواْ بَلۡ نَتَّبِعُ مَآ أَلۡفَيۡنَا عَلَيۡهِ ءَابَآءَنَآۚ أَوَلَوۡ كَانَ ءَابَآؤُهُمۡ لَا يَعۡقِلُونَ شَيۡـٔٗا وَلَا يَهۡتَدُونَ ﴾
[البَقَرَة: 170]

Ndipo pamene zimanenedwa kwa iwo kuti: Tsatirani zimene Mulungu wavumbulutsa, iwo amayankha: “Iyayi, ife tidzatsatira zimene tidapeza makolo athu ali kuchita.” Ngakhale kuti makolo awo adali osadziwa kapena osowa chilangizo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا قيل لهم اتبعوا ما أنـزل الله قالوا بل نتبع ما ألفينا, باللغة نيانجا

﴿وإذا قيل لهم اتبعوا ما أنـزل الله قالوا بل نتبع ما ألفينا﴾ [البَقَرَة: 170]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo kukanenedwa kwa iwo (kuti): “Tsatirani zimene Allah wavumbulutsa;” akunena: “Koma tikutsatira zimene tidawapeza nazo atate athu.” Kodi ngakhale kuti atate awo sadali kuzindikira chilichonse ndiponso sadali oongoka (awatsatirabe)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek