×

oh inu anthu okhulupirira! Kusala kudalamulidwa kwa inu monga momwe kudalamulidwa kwa 2:183 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:183) ayat 183 in Chichewa

2:183 Surah Al-Baqarah ayat 183 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 183 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ كُتِبَ عَلَيۡكُمُ ٱلصِّيَامُ كَمَا كُتِبَ عَلَى ٱلَّذِينَ مِن قَبۡلِكُمۡ لَعَلَّكُمۡ تَتَّقُونَ ﴾
[البَقَرَة: 183]

oh inu anthu okhulupirira! Kusala kudalamulidwa kwa inu monga momwe kudalamulidwa kwa iwo amene adalipo kalero inu musanadze kuti inu mukhale woyera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا كتب عليكم الصيام كما كتب على الذين من قبلكم, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا كتب عليكم الصيام كما كتب على الذين من قبلكم﴾ [البَقَرَة: 183]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Kwalamulidwa kwa inu kusala (m’mwezi wa Ramadan) monga momwe kudalamulidwira kwa anthu akale, inu musadabwere kuti muope Allah (popewa zoletsedwa)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek