×

Koma iye amene aopa kuti munthu wochitira umboni akhoza kukondera kapena kulakwa 2:182 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:182) ayat 182 in Chichewa

2:182 Surah Al-Baqarah ayat 182 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 182 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿فَمَنۡ خَافَ مِن مُّوصٖ جَنَفًا أَوۡ إِثۡمٗا فَأَصۡلَحَ بَيۡنَهُمۡ فَلَآ إِثۡمَ عَلَيۡهِۚ إِنَّ ٱللَّهَ غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[البَقَرَة: 182]

Koma iye amene aopa kuti munthu wochitira umboni akhoza kukondera kapena kulakwa ndipo abweretsa chiweruzo chabwino pakati pa anthu otsutsana, iye sali wolakwa pa china chilichonse. Ndithudi Mulungu ndi wokhululukira ndi wachisoni chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فمن خاف من موص جنفا أو إثما فأصلح بينهم فلا إثم عليه, باللغة نيانجا

﴿فمن خاف من موص جنفا أو إثما فأصلح بينهم فلا إثم عليه﴾ [البَقَرَة: 182]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene waopa kuti wopereka wasiya angapendekere kumbali yokhota kapena ku uchimo, nalinganiza pakati pawo, palibe tchimo kwa iye. Ndithudi, Allah ngokhululuka zedi, Ngwachifundo chambiri
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek