×

Nthawi ya Hajji ili ndi miyezi yake yodziwika. Aliyense amene afuna kupanga 2:197 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:197) ayat 197 in Chichewa

2:197 Surah Al-Baqarah ayat 197 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 197 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿ٱلۡحَجُّ أَشۡهُرٞ مَّعۡلُومَٰتٞۚ فَمَن فَرَضَ فِيهِنَّ ٱلۡحَجَّ فَلَا رَفَثَ وَلَا فُسُوقَ وَلَا جِدَالَ فِي ٱلۡحَجِّۗ وَمَا تَفۡعَلُواْ مِنۡ خَيۡرٖ يَعۡلَمۡهُ ٱللَّهُۗ وَتَزَوَّدُواْ فَإِنَّ خَيۡرَ ٱلزَّادِ ٱلتَّقۡوَىٰۖ وَٱتَّقُونِ يَٰٓأُوْلِي ٱلۡأَلۡبَٰبِ ﴾
[البَقَرَة: 197]

Nthawi ya Hajji ili ndi miyezi yake yodziwika. Aliyense amene afuna kupanga Hajji m’menemu sayenera kugona ndi mkazi wake kapena kuchitazoipakapenakukanganandianzakenthawiya Hajji. Ndipo chabwino chilichonse chimene muchita, Mulungu amachidziwa. Mutenge kamba wa paulendo, koma kamba wabwino ndi kuopa Mulungu. Motero ndiopeni Ine, inu anthu ozindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الحج أشهر معلومات فمن فرض فيهن الحج فلا رفث ولا فسوق ولا, باللغة نيانجا

﴿الحج أشهر معلومات فمن فرض فيهن الحج فلا رفث ولا فسوق ولا﴾ [البَقَرَة: 197]

Khaled Ibrahim Betala
“(Mapemphero a) Hajj ali ndi miyezi yodziwika, (yomwe ndi: Shawwal, Dhul Qa’da ndi Dhul Hijjah). Amene watsimikiza kuchita Hajj m’miyezi imeneyo, asachite ndi kuyankhula zauve, ndiponso asapandukire malamulo (pochita zoletsedwa uku iye ali m’mapemphero a Hajj), ndiponso asakangane ali m’Hajjimo. Ndipo chabwino chilichonse chimene mungachite, Allah achidziwa. Ndipo dzikonzereni kamba wa paulendo, ndithu kamba wabwino (wadziko lapansi) ndi amene angakupewetseni kupemphapempha, (koma kamba wabwino wa tsiku lachimaliziro ndiko kuopa Allah). Choncho ndiopeni inu eni nzeru
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek