×

Ndipo zikanenedwa kwa iye kuti: “Opa Mulungu,” kudzitukumula kwake kumamupangitsa kuchita zoipa. 2:206 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:206) ayat 206 in Chichewa

2:206 Surah Al-Baqarah ayat 206 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 206 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿وَإِذَا قِيلَ لَهُ ٱتَّقِ ٱللَّهَ أَخَذَتۡهُ ٱلۡعِزَّةُ بِٱلۡإِثۡمِۚ فَحَسۡبُهُۥ جَهَنَّمُۖ وَلَبِئۡسَ ٱلۡمِهَادُ ﴾
[البَقَرَة: 206]

Ndipo zikanenedwa kwa iye kuti: “Opa Mulungu,” kudzitukumula kwake kumamupangitsa kuchita zoipa. Motero Gahena ndi yomuyenera. Ndipo ndi malo oipa kupumirako

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا قيل له اتق الله أخذته العزة بالإثم فحسبه جهنم ولبئس المهاد, باللغة نيانجا

﴿وإذا قيل له اتق الله أخذته العزة بالإثم فحسبه جهنم ولبئس المهاد﴾ [البَقَرَة: 206]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akauzidwa kuti: “Opa Allah”, Akugwidwa ndi mwano womupititsa ku machimo, choncho Jahannam ikukwana kwa iye (kuwuchotsa mwano wakewo). Taonani kuipa kwa malo wokakhazikikamo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek