×

Ndipo pamene iye achoka, amapita uku ndi uku kuyambitsa chisokonezo m’dziko ndi 2:205 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:205) ayat 205 in Chichewa

2:205 Surah Al-Baqarah ayat 205 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 205 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿وَإِذَا تَوَلَّىٰ سَعَىٰ فِي ٱلۡأَرۡضِ لِيُفۡسِدَ فِيهَا وَيُهۡلِكَ ٱلۡحَرۡثَ وَٱلنَّسۡلَۚ وَٱللَّهُ لَا يُحِبُّ ٱلۡفَسَادَ ﴾
[البَقَرَة: 205]

Ndipo pamene iye achoka, amapita uku ndi uku kuyambitsa chisokonezo m’dziko ndi kuononga mbeu ndi ng’ombe ndipo Mulungu sakonda chisokonezo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا تولى سعى في الأرض ليفسد فيها ويهلك الحرث والنسل والله لا, باللغة نيانجا

﴿وإذا تولى سعى في الأرض ليفسد فيها ويهلك الحرث والنسل والله لا﴾ [البَقَرَة: 205]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma akachoka (kwa iwe) akuyenda pa dziko (uku ndi uku) ncholinga chofuna kuyipitsapo ndi kuononga zomera ndi miyoyo. Komatu Allah sakonda kuononga
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek