×

Ndipo ngati inu muterera ndi kubwerera m’mbuyo pamene zizindikiro zadza kwa inu, 2:209 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:209) ayat 209 in Chichewa

2:209 Surah Al-Baqarah ayat 209 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 209 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿فَإِن زَلَلۡتُم مِّنۢ بَعۡدِ مَا جَآءَتۡكُمُ ٱلۡبَيِّنَٰتُ فَٱعۡلَمُوٓاْ أَنَّ ٱللَّهَ عَزِيزٌ حَكِيمٌ ﴾
[البَقَرَة: 209]

Ndipo ngati inu muterera ndi kubwerera m’mbuyo pamene zizindikiro zadza kwa inu, dziwani kuti Mulungu ndi wa Mphamvu ndi Wanzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فإن زللتم من بعد ما جاءتكم البينات فاعلموا أن الله عزيز حكيم, باللغة نيانجا

﴿فإن زللتم من بعد ما جاءتكم البينات فاعلموا أن الله عزيز حكيم﴾ [البَقَرَة: 209]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ngati mutaterezuka (kuchimwa) pambuyo pokudzerani zisonyezo (za Allah) zoonekera poyera, dziwani kuti Allah Ngwamphamvu zoposa; Ngwanzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek