Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 210 - البَقَرَة - Page - Juz 2
﴿هَلۡ يَنظُرُونَ إِلَّآ أَن يَأۡتِيَهُمُ ٱللَّهُ فِي ظُلَلٖ مِّنَ ٱلۡغَمَامِ وَٱلۡمَلَٰٓئِكَةُ وَقُضِيَ ٱلۡأَمۡرُۚ وَإِلَى ٱللَّهِ تُرۡجَعُ ٱلۡأُمُورُ ﴾
[البَقَرَة: 210]
﴿هل ينظرون إلا أن يأتيهم الله في ظلل من الغمام والملائكة وقضي﴾ [البَقَرَة: 210]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi pali china chimene akuyembekeza posakhala kuwadzera Allah m’mithunzi ya mitambo ndi (kuwadzera) angelo; nkuweruzidwa chilamulo (chakuonongeka kwawo)? Komatu zinthu zonse zimabwezedwa kwa Allah |