×

Akazi anu ndi minda yanu kotero lowani m’minda yanu monga momwe mufunira, 2:223 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:223) ayat 223 in Chichewa

2:223 Surah Al-Baqarah ayat 223 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 223 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿نِسَآؤُكُمۡ حَرۡثٞ لَّكُمۡ فَأۡتُواْ حَرۡثَكُمۡ أَنَّىٰ شِئۡتُمۡۖ وَقَدِّمُواْ لِأَنفُسِكُمۡۚ وَٱتَّقُواْ ٱللَّهَ وَٱعۡلَمُوٓاْ أَنَّكُم مُّلَٰقُوهُۗ وَبَشِّرِ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[البَقَرَة: 223]

Akazi anu ndi minda yanu kotero lowani m’minda yanu monga momwe mufunira, dzitsogozereni nokha ntchito zabwino. Ndipo muopeni Mulungu, ndipo dziwani kuti mudzakumana naye. Ndipo pelekani nkhani yabwino kwa anthu okhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: نساؤكم حرث لكم فأتوا حرثكم أنى شئتم وقدموا لأنفسكم واتقوا الله واعلموا, باللغة نيانجا

﴿نساؤكم حرث لكم فأتوا حرثكم أنى شئتم وقدموا لأنفسكم واتقوا الله واعلموا﴾ [البَقَرَة: 223]

Khaled Ibrahim Betala
“Akazi anu ali ngati minda yanu; choncho idzereni minda yanu mmene mungafunire; koma dzitsogozereni zabwino nokha, ndipo opani Allah, ndipo dziwaninso kuti mudzakumana naye. Ndipo auze nkhani yabwino amene akhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek