×

Iwo amene amalumbira kuti sadzakhala malo amodzi ndi akazi awo adikire miyezi 2:226 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:226) ayat 226 in Chichewa

2:226 Surah Al-Baqarah ayat 226 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 226 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿لِّلَّذِينَ يُؤۡلُونَ مِن نِّسَآئِهِمۡ تَرَبُّصُ أَرۡبَعَةِ أَشۡهُرٖۖ فَإِن فَآءُو فَإِنَّ ٱللَّهَ غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[البَقَرَة: 226]

Iwo amene amalumbira kuti sadzakhala malo amodzi ndi akazi awo adikire miyezi inayi, ndipo ngati iwo abwererana, ndithudi, Mulungu ndi wokhululukira ndi wachifundo chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: للذين يؤلون من نسائهم تربص أربعة أشهر فإن فاءوا فإن الله غفور, باللغة نيانجا

﴿للذين يؤلون من نسائهم تربص أربعة أشهر فإن فاءوا فإن الله غفور﴾ [البَقَرَة: 226]

Khaled Ibrahim Betala
“Kwa omwe akulumbilira kuti adzipatula kwa akazi awo, (nyengo yawo) ayembekezere miyezi inayi. Koma ngati atabwerera (nakhala pamodzi ndi akazi awo), ndithudi Allah Ngokhululuka kwambiri, Ngwachisoni zedi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek