×

Mulungu sadzakulangani chifukwa cha kuphwanya mwangozi malonjezo anu amene mudachita. Koma adzakulangani 2:225 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:225) ayat 225 in Chichewa

2:225 Surah Al-Baqarah ayat 225 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 225 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿لَّا يُؤَاخِذُكُمُ ٱللَّهُ بِٱللَّغۡوِ فِيٓ أَيۡمَٰنِكُمۡ وَلَٰكِن يُؤَاخِذُكُم بِمَا كَسَبَتۡ قُلُوبُكُمۡۗ وَٱللَّهُ غَفُورٌ حَلِيمٞ ﴾
[البَقَرَة: 225]

Mulungu sadzakulangani chifukwa cha kuphwanya mwangozi malonjezo anu amene mudachita. Koma adzakulangani pa zinthu zimene mitima yanu yachita ndipo Mulungu ndi wokhululukira ndi wopirira kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لا يؤاخذكم الله باللغو في أيمانكم ولكن يؤاخذكم بما كسبت قلوبكم والله, باللغة نيانجا

﴿لا يؤاخذكم الله باللغو في أيمانكم ولكن يؤاخذكم بما كسبت قلوبكم والله﴾ [البَقَرَة: 225]

Khaled Ibrahim Betala
“Allah sangakulangeni pa kulumbira kwanu kopanda pake, koma adzakulangani chifukwa cha malumbiro anu amene mitima yanu yatsimikiza mwa mphamvu. Ndipo Allah Ngokhululuka kwabasi, Ngoleza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek