×

Mulungu! Kulibe mulungu wina koma Iye yekha, wamoyo ndi wamuyaya. Iye saodzera 2:255 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:255) ayat 255 in Chichewa

2:255 Surah Al-Baqarah ayat 255 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 255 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿ٱللَّهُ لَآ إِلَٰهَ إِلَّا هُوَ ٱلۡحَيُّ ٱلۡقَيُّومُۚ لَا تَأۡخُذُهُۥ سِنَةٞ وَلَا نَوۡمٞۚ لَّهُۥ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَمَا فِي ٱلۡأَرۡضِۗ مَن ذَا ٱلَّذِي يَشۡفَعُ عِندَهُۥٓ إِلَّا بِإِذۡنِهِۦۚ يَعۡلَمُ مَا بَيۡنَ أَيۡدِيهِمۡ وَمَا خَلۡفَهُمۡۖ وَلَا يُحِيطُونَ بِشَيۡءٖ مِّنۡ عِلۡمِهِۦٓ إِلَّا بِمَا شَآءَۚ وَسِعَ كُرۡسِيُّهُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَۖ وَلَا يَـُٔودُهُۥ حِفۡظُهُمَاۚ وَهُوَ ٱلۡعَلِيُّ ٱلۡعَظِيمُ ﴾
[البَقَرَة: 255]

Mulungu! Kulibe mulungu wina koma Iye yekha, wamoyo ndi wamuyaya. Iye saodzera kapena kugona. Zake ndi zonse zimene zili kumwamba ndi padziko lapansi. Ndani amene angakhale mkhalapakati pa Iye opanda chilolezo chake? Iye amadziwa zonse zimene zimachitika mdziko lino ndi zimene zidzachitike m’moyo uli nkudza. Ndipo iwo sadzadziwa chilichonse kuchokera ku nzeru zake pokhapokha ngati Iye afuna. Mpando wake umafika kumwamba ndi dziko lapansi. Ndipo chisamaliro chake pazinthu zonse sichimutopetsa ayi. Iye ndi wapamwamba mwamba ndi Wamkulu zedi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الله لا إله إلا هو الحي القيوم لا تأخذه سنة ولا نوم, باللغة نيانجا

﴿الله لا إله إلا هو الحي القيوم لا تأخذه سنة ولا نوم﴾ [البَقَرَة: 255]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek