×

Palibe kukakamizana m’chipembedzo. Ndithudi njira yoyenera yaonekera kusiyana ndi njira yolakwa. Iye 2:256 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:256) ayat 256 in Chichewa

2:256 Surah Al-Baqarah ayat 256 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 256 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿لَآ إِكۡرَاهَ فِي ٱلدِّينِۖ قَد تَّبَيَّنَ ٱلرُّشۡدُ مِنَ ٱلۡغَيِّۚ فَمَن يَكۡفُرۡ بِٱلطَّٰغُوتِ وَيُؤۡمِنۢ بِٱللَّهِ فَقَدِ ٱسۡتَمۡسَكَ بِٱلۡعُرۡوَةِ ٱلۡوُثۡقَىٰ لَا ٱنفِصَامَ لَهَاۗ وَٱللَّهُ سَمِيعٌ عَلِيمٌ ﴾
[البَقَرَة: 256]

Palibe kukakamizana m’chipembedzo. Ndithudi njira yoyenera yaonekera kusiyana ndi njira yolakwa. Iye amene asiya kupembedza mafano ndipo aika chikhulupiriro chake mwa Mulungu, ndithudi wagwiritsitsa chingwe chimene sichidzaduka. Ndipo Mulungu ndi wakumva ndi wodziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لا إكراه في الدين قد تبين الرشد من الغي فمن يكفر بالطاغوت, باللغة نيانجا

﴿لا إكراه في الدين قد تبين الرشد من الغي فمن يكفر بالطاغوت﴾ [البَقَرَة: 256]

Khaled Ibrahim Betala
“Palibe kukakamiza (munthu kulowa) m’chipembedzo; kulungama kwaonekera poyera kusiyana ndi kusalungama. Choncho amene akumkana satana nakhulupirira Allah, ndiye kuti wagwira chigwiliro cholimba, chomwe sichisweka. Ndipo Allah Ngwakumva; Ngodziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek