×

Kuulula chimene mwapereka ndi bwino koma kupereka mwa mseri kwa anthu osauka 2:271 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:271) ayat 271 in Chichewa

2:271 Surah Al-Baqarah ayat 271 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 271 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿إِن تُبۡدُواْ ٱلصَّدَقَٰتِ فَنِعِمَّا هِيَۖ وَإِن تُخۡفُوهَا وَتُؤۡتُوهَا ٱلۡفُقَرَآءَ فَهُوَ خَيۡرٞ لَّكُمۡۚ وَيُكَفِّرُ عَنكُم مِّن سَيِّـَٔاتِكُمۡۗ وَٱللَّهُ بِمَا تَعۡمَلُونَ خَبِيرٞ ﴾
[البَقَرَة: 271]

Kuulula chimene mwapereka ndi bwino koma kupereka mwa mseri kwa anthu osauka ndi kwabwino kwambiri. Mulungu adzakukhululukirani ena mwa machimo anu. Ndipo Mulungu amadziwa chinthu china chilichonse chimene mumachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن تبدوا الصدقات فنعما هي وإن تخفوها وتؤتوها الفقراء فهو خير لكم, باللغة نيانجا

﴿إن تبدوا الصدقات فنعما هي وإن تخفوها وتؤتوها الفقراء فهو خير لكم﴾ [البَقَرَة: 271]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati mupereka sadaka moonetsera, ndibwino; ngati mungaipereke mobisa, ndikuipereka kwa osauka, umenewo ndiubwino woposa kwa inu. Ndipo akufafanizirani zoipa zanu (ngati mutero). Ndipo Allah akudziwa zonse zimene mukuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek