×

Mwini wa zonse zimene zili kumwamba ndi pa dziko lapansi ndi Mulungu. 2:284 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:284) ayat 284 in Chichewa

2:284 Surah Al-Baqarah ayat 284 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 284 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿لِّلَّهِ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَمَا فِي ٱلۡأَرۡضِۗ وَإِن تُبۡدُواْ مَا فِيٓ أَنفُسِكُمۡ أَوۡ تُخۡفُوهُ يُحَاسِبۡكُم بِهِ ٱللَّهُۖ فَيَغۡفِرُ لِمَن يَشَآءُ وَيُعَذِّبُ مَن يَشَآءُۗ وَٱللَّهُ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٌ ﴾
[البَقَرَة: 284]

Mwini wa zonse zimene zili kumwamba ndi pa dziko lapansi ndi Mulungu. Kaya inu muulula za m’maganizo anu kapena mubisa, Mulungu adzakufunsani za izo. Iye amakhululukira aliyense amene Iye wamufuna ndipo amalanga aliyense amene Iye wamufuna . Mulungu ali ndi mphamvu pa chinthu china chili chonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لله ما في السموات وما في الأرض وإن تبدوا ما في أنفسكم, باللغة نيانجا

﴿لله ما في السموات وما في الأرض وإن تبدوا ما في أنفسكم﴾ [البَقَرَة: 284]

Khaled Ibrahim Betala
“Zonse zakumwamba ndi zapansi nza Allah. Kaya muonetsera poyera zomwe zili m’mitima mwanu kapena kuzibisa, Allah adzakuchitirani nazo chiwerengero. Kenako adzakhululukira amene wamfuna (atalapa). Ndipo adzamlanga amene wamfuna (akapanda kulapa). Ndipo Allah Ngokhoza chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek