×

Mulungu sapereka katundu wolemera pa mzimu umene siungathe kumunyamula. Mzimuuliwonseumalandirachilichonsechabwinochimene umachita kapena 2:286 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:286) ayat 286 in Chichewa

2:286 Surah Al-Baqarah ayat 286 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 286 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿لَا يُكَلِّفُ ٱللَّهُ نَفۡسًا إِلَّا وُسۡعَهَاۚ لَهَا مَا كَسَبَتۡ وَعَلَيۡهَا مَا ٱكۡتَسَبَتۡۗ رَبَّنَا لَا تُؤَاخِذۡنَآ إِن نَّسِينَآ أَوۡ أَخۡطَأۡنَاۚ رَبَّنَا وَلَا تَحۡمِلۡ عَلَيۡنَآ إِصۡرٗا كَمَا حَمَلۡتَهُۥ عَلَى ٱلَّذِينَ مِن قَبۡلِنَاۚ رَبَّنَا وَلَا تُحَمِّلۡنَا مَا لَا طَاقَةَ لَنَا بِهِۦۖ وَٱعۡفُ عَنَّا وَٱغۡفِرۡ لَنَا وَٱرۡحَمۡنَآۚ أَنتَ مَوۡلَىٰنَا فَٱنصُرۡنَا عَلَى ٱلۡقَوۡمِ ٱلۡكَٰفِرِينَ ﴾
[البَقَرَة: 286]

Mulungu sapereka katundu wolemera pa mzimu umene siungathe kumunyamula. Mzimuuliwonseumalandirachilichonsechabwinochimene umachita kapena umalangidwa chifukwa cha ntchito zake zoipa zimene umachita. Pemphani kuti: “Ambuye wathu! Musatilange ife ngati tiiwala kapena tilakwa. Ambuye wathu! Musatikundikire ife mavuto monga amene mudakundikira anthu amene adalipo kale. Ambuye wathu! Musatisenzetse zinthu zimene sitingathe kuzinyamula. Tichotsereni machimo, tikhululukireni ndipo tichitireni chifundo ife. Inu nokha ndinu Mtetezi wathu. Tipatseni kupambana pakati pa anthu osakhulupirira.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لا يكلف الله نفسا إلا وسعها لها ما كسبت وعليها ما اكتسبت, باللغة نيانجا

﴿لا يكلف الله نفسا إلا وسعها لها ما كسبت وعليها ما اكتسبت﴾ [البَقَرَة: 286]

Khaled Ibrahim Betala
“Allah sakakamiza mzimu uliwonse koma chimene chili cholingana ndi kukhoza kwake. (Ndipo phindu la) zimene mzimuwo udapeza ndilake ndiponso kuluza kwa zomwe udapeza nkwake. (Asilamuwo amanena) “E Mbuye wathu! Musatilange tikaiwala kapena tikalakwitsa, E Mbuye wathu! Musatisenzetse mtolo (wamalamulo) monga munawasenzetsera amene adalipo patsogolo pathu. E Mbuye wathu! Musatisenzetse chimene sitingachithe. Tifafanizireni machimo athu, tikhululukireni zolakwa zathu, ndiponso tichitireni chifundo. Inu Ndinu Mtetezi wathu. Choncho tithangateni ku anthu osakhulupirira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek