×

Ndipo Iye adamuphunzitsa Adamu mayina a zinthu zonse ndipo adazisonkhanitsa pamaso pa 2:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:31) ayat 31 in Chichewa

2:31 Surah Al-Baqarah ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 31 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَعَلَّمَ ءَادَمَ ٱلۡأَسۡمَآءَ كُلَّهَا ثُمَّ عَرَضَهُمۡ عَلَى ٱلۡمَلَٰٓئِكَةِ فَقَالَ أَنۢبِـُٔونِي بِأَسۡمَآءِ هَٰٓؤُلَآءِ إِن كُنتُمۡ صَٰدِقِينَ ﴾
[البَقَرَة: 31]

Ndipo Iye adamuphunzitsa Adamu mayina a zinthu zonse ndipo adazisonkhanitsa pamaso pa angelo nati: “Ndiuzeni mayina a zinthu izi ngati ndinu achilungamo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وعلم آدم الأسماء كلها ثم عرضهم على الملائكة فقال أنبئوني بأسماء هؤلاء, باللغة نيانجا

﴿وعلم آدم الأسماء كلها ثم عرضهم على الملائكة فقال أنبئوني بأسماء هؤلاء﴾ [البَقَرَة: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (Allah) adaphunzitsa Adam mayina a (zinthu) zonse; nazibweretsa (zinthuzo) pamaso pa Angelo, naati (kwa Angelo): “Ndiuzeni mayina a zinthu izi ngati mukunena zoona (kuti inu ndinu ozindikira zinthu).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek