×

Ndipo Ife tidati: “oh Adamu! Khala iwe pamodzi ndi mkazi wako m’mundamo 2:35 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:35) ayat 35 in Chichewa

2:35 Surah Al-Baqarah ayat 35 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 35 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَقُلۡنَا يَٰٓـَٔادَمُ ٱسۡكُنۡ أَنتَ وَزَوۡجُكَ ٱلۡجَنَّةَ وَكُلَا مِنۡهَا رَغَدًا حَيۡثُ شِئۡتُمَا وَلَا تَقۡرَبَا هَٰذِهِ ٱلشَّجَرَةَ فَتَكُونَا مِنَ ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[البَقَرَة: 35]

Ndipo Ife tidati: “oh Adamu! Khala iwe pamodzi ndi mkazi wako m’mundamo ndipo muzidya mmene mungafunire koma musadzayandikire mtengo uwu chifukwa mudzakhala anthu ochimwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقلنا ياآدم اسكن أنت وزوجك الجنة وكلا منها رغدا حيث شئتما ولا, باللغة نيانجا

﴿وقلنا ياآدم اسكن أنت وزوجك الجنة وكلا منها رغدا حيث شئتما ولا﴾ [البَقَرَة: 35]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tidati: “E iwe Adam! Khala iwe ndi mkazi wako m’mundamo (mu Edeni); idyani m’menemo motakasuka paliponse pamene mwafuna; koma musauyandikire Mtengo uwu kuopera kuti mungakhale mwa odzichitira okha zoipa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek