×

Ife tidati: “Tsikani pansi nonsenu ndipo pamene Ulangizi wanga udzakufikani, yense amene 2:38 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:38) ayat 38 in Chichewa

2:38 Surah Al-Baqarah ayat 38 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 38 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿قُلۡنَا ٱهۡبِطُواْ مِنۡهَا جَمِيعٗاۖ فَإِمَّا يَأۡتِيَنَّكُم مِّنِّي هُدٗى فَمَن تَبِعَ هُدَايَ فَلَا خَوۡفٌ عَلَيۡهِمۡ وَلَا هُمۡ يَحۡزَنُونَ ﴾
[البَقَرَة: 38]

Ife tidati: “Tsikani pansi nonsenu ndipo pamene Ulangizi wanga udzakufikani, yense amene adzatsatira Ulangiziwu, iye sadzakhala ndi mantha ndipo sadzadandaula.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قلنا اهبطوا منها جميعا فإما يأتينكم مني هدى فمن تبع هداي فلا, باللغة نيانجا

﴿قلنا اهبطوا منها جميعا فإما يأتينكم مني هدى فمن تبع هداي فلا﴾ [البَقَرَة: 38]

Khaled Ibrahim Betala
“Tidati: “Tsikani m’menemo nonsenu. Ngati chitakufikani chiongoko chochokera kwa Ine, choncho amene adzatsate chiongoko Changacho, pa iwo sipadzakhala mantha. Ndiponso iwo sadzadandaula.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek