×

Ndi pamene tidawauza kuti: Lowani mu Mzinda uwu ndipo mudye mmenemo mosangalala 2:58 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:58) ayat 58 in Chichewa

2:58 Surah Al-Baqarah ayat 58 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 58 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَإِذۡ قُلۡنَا ٱدۡخُلُواْ هَٰذِهِ ٱلۡقَرۡيَةَ فَكُلُواْ مِنۡهَا حَيۡثُ شِئۡتُمۡ رَغَدٗا وَٱدۡخُلُواْ ٱلۡبَابَ سُجَّدٗا وَقُولُواْ حِطَّةٞ نَّغۡفِرۡ لَكُمۡ خَطَٰيَٰكُمۡۚ وَسَنَزِيدُ ٱلۡمُحۡسِنِينَ ﴾
[البَقَرَة: 58]

Ndi pamene tidawauza kuti: Lowani mu Mzinda uwu ndipo mudye mmenemo mosangalala ndi momwe mungafunire. Lowani modzichepetsa pachipata ndipo munene kuti: “Tikhululukireni” ndipo Ife tidzakukhululukirani machimo anu ndipo tidzawaonjezera zabwino anthu onse ochita zabwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذ قلنا ادخلوا هذه القرية فكلوا منها حيث شئتم رغدا وادخلوا الباب, باللغة نيانجا

﴿وإذ قلنا ادخلوا هذه القرية فكلوا منها حيث شئتم رغدا وادخلوا الباب﴾ [البَقَرَة: 58]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (kumbukiraninso nkhani iyi) pamene tidati: “Lowani m’mudzi uwu, ndikudya m’menemo motakasuka paliponse pamene mwafuna; ndipo lowerani pachipata chake uku mutawerama (kusonyeza kuthokoza Allah) ndipo nenani: “E Mbuye wathu! Tikhululukireni machimo athu.” “Tikukhululukirani machimo anu ndipo tiwaonjezera (mphoto yaikulu) ochita zabwino.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek