×

Koma anthu ochita zoipa adasintha mawu amene adanenedwa kwa iwo ndipo tidawaponyera, 2:59 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:59) ayat 59 in Chichewa

2:59 Surah Al-Baqarah ayat 59 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 59 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿فَبَدَّلَ ٱلَّذِينَ ظَلَمُواْ قَوۡلًا غَيۡرَ ٱلَّذِي قِيلَ لَهُمۡ فَأَنزَلۡنَا عَلَى ٱلَّذِينَ ظَلَمُواْ رِجۡزٗا مِّنَ ٱلسَّمَآءِ بِمَا كَانُواْ يَفۡسُقُونَ ﴾
[البَقَرَة: 59]

Koma anthu ochita zoipa adasintha mawu amene adanenedwa kwa iwo ndipo tidawaponyera, ngati chilango, mlili ochokera kumwamba chifukwa cha zolakwa zawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فبدل الذين ظلموا قولا غير الذي قيل لهم فأنـزلنا على الذين ظلموا, باللغة نيانجا

﴿فبدل الذين ظلموا قولا غير الذي قيل لهم فأنـزلنا على الذين ظلموا﴾ [البَقَرَة: 59]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma anthu oipa adasintha (lamulo la Allah, nanena) mawu ena osati amene adawuzidwa. Tero, anthu oipawo tidawatsitsira mliri wochokera kumwamba, chifukwa chakutuluka kwawo m’chilamulo cha Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek