×

Ndipo zitatero inu mudabwerera m’mbuyo. Koma pakadapanda chisomo ndi chisoni cha Mulungu 2:64 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:64) ayat 64 in Chichewa

2:64 Surah Al-Baqarah ayat 64 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 64 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿ثُمَّ تَوَلَّيۡتُم مِّنۢ بَعۡدِ ذَٰلِكَۖ فَلَوۡلَا فَضۡلُ ٱللَّهِ عَلَيۡكُمۡ وَرَحۡمَتُهُۥ لَكُنتُم مِّنَ ٱلۡخَٰسِرِينَ ﴾
[البَقَرَة: 64]

Ndipo zitatero inu mudabwerera m’mbuyo. Koma pakadapanda chisomo ndi chisoni cha Mulungu pa inu, ndithudi inu mukadakhala mgulu la anthu osochera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ثم توليتم من بعد ذلك فلولا فضل الله عليكم ورحمته لكنتم من, باللغة نيانجا

﴿ثم توليتم من بعد ذلك فلولا فضل الله عليكم ورحمته لكنتم من﴾ [البَقَرَة: 64]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma pambuyo pazimenezo mudatembenuka ndikunyoza. Pakadapanda ubwino wa Allah ndi chifundo chake pa inu, mukadakhala mwa otayika (oonongeka pa dziko lapansi)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek