×

Ndipo, ndithudi, inu mudadziwa za anthu amene adaswa malamulo a tsiku la 2:65 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:65) ayat 65 in Chichewa

2:65 Surah Al-Baqarah ayat 65 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 65 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَلَقَدۡ عَلِمۡتُمُ ٱلَّذِينَ ٱعۡتَدَوۡاْ مِنكُمۡ فِي ٱلسَّبۡتِ فَقُلۡنَا لَهُمۡ كُونُواْ قِرَدَةً خَٰسِـِٔينَ ﴾
[البَقَرَة: 65]

Ndipo, ndithudi, inu mudadziwa za anthu amene adaswa malamulo a tsiku la Sabata. Ife tidawauza kuti: “Khalani anyani, onyozedwa ndi okanidwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد علمتم الذين اعتدوا منكم في السبت فقلنا لهم كونوا قردة خاسئين, باللغة نيانجا

﴿ولقد علمتم الذين اعتدوا منكم في السبت فقلنا لهم كونوا قردة خاسئين﴾ [البَقَرَة: 65]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi mudawadziwa (anthu) amene adapyola malire mwa inu pakuswa kupatulika kwa tsiku la Sabata (m’mene tidawalangira chifukwa chosodza nsomba pa tsiku loletsedwa). Ndipo tidati kwa iwo: “Khalani anyani onyozeka.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek