Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 66 - البَقَرَة - Page - Juz 1
﴿فَجَعَلۡنَٰهَا نَكَٰلٗا لِّمَا بَيۡنَ يَدَيۡهَا وَمَا خَلۡفَهَا وَمَوۡعِظَةٗ لِّلۡمُتَّقِينَ ﴾ 
[البَقَرَة: 66]
﴿فجعلناها نكالا لما بين يديها وما خلفها وموعظة للمتقين﴾ [البَقَرَة: 66]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tidakuchita kukhala anyaniko, chilango chochenjeza amene adalipo pa nthawiyo ndi akudza pambuyo pawo, ndiponso phunziro kwa oopa Allah |