×

Mulungu waika chophimba m’mitima mwawo ndi m’makutu mwawo, ndi m’maso mwawo muli 2:7 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:7) ayat 7 in Chichewa

2:7 Surah Al-Baqarah ayat 7 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 7 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿خَتَمَ ٱللَّهُ عَلَىٰ قُلُوبِهِمۡ وَعَلَىٰ سَمۡعِهِمۡۖ وَعَلَىٰٓ أَبۡصَٰرِهِمۡ غِشَٰوَةٞۖ وَلَهُمۡ عَذَابٌ عَظِيمٞ ﴾
[البَقَرَة: 7]

Mulungu waika chophimba m’mitima mwawo ndi m’makutu mwawo, ndi m’maso mwawo muli chovindikira. Ndipo chawo chidzakhala chilango chachikulu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ختم الله على قلوبهم وعلى سمعهم وعلى أبصارهم غشاوة ولهم عذاب عظيم, باللغة نيانجا

﴿ختم الله على قلوبهم وعلى سمعهم وعلى أبصارهم غشاوة ولهم عذاب عظيم﴾ [البَقَرَة: 7]

Khaled Ibrahim Betala
“(Ali ngati kuti) Allah wawadinda chidindo chotseka mitima yawo ndi makutu awo (kotero kuti kuunika kwa chikhulupiliro sikungalowemo), ndipo m’maso mwawo muli chophimba (sangathe kuona zozizwitsa za Allah); choncho iwo adzalandira chilango chachikulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek