×

Iwo adati: “Ife sitidzakhudzidwa ndi moto kupatula masiku owerengeka okha”. Nena: “Kodi 2:80 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:80) ayat 80 in Chichewa

2:80 Surah Al-Baqarah ayat 80 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 80 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَقَالُواْ لَن تَمَسَّنَا ٱلنَّارُ إِلَّآ أَيَّامٗا مَّعۡدُودَةٗۚ قُلۡ أَتَّخَذۡتُمۡ عِندَ ٱللَّهِ عَهۡدٗا فَلَن يُخۡلِفَ ٱللَّهُ عَهۡدَهُۥٓۖ أَمۡ تَقُولُونَ عَلَى ٱللَّهِ مَا لَا تَعۡلَمُونَ ﴾
[البَقَرَة: 80]

Iwo adati: “Ife sitidzakhudzidwa ndi moto kupatula masiku owerengeka okha”. Nena: “Kodi inu mwapanga lonjezo ndi Mulungu limene Iye sadzaphwanya? Kapena kodi inu mumanena zinthu zokhudzana Mulungu zimene simuzidziwa?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقالوا لن تمسنا النار إلا أياما معدودة قل أتخذتم عند الله عهدا, باللغة نيانجا

﴿وقالوا لن تمسنا النار إلا أياما معدودة قل أتخذتم عند الله عهدا﴾ [البَقَرَة: 80]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akunena: “Sudzatikhudza Moto kupatula masiku owerengeka basi.”Auze: “Kodi mudapangana naye Allah, kuti potero sadzaswa lonjezo Lake, kapena mukungomunenera Allah zimene simukuzidziwa?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek