×

Ndipo pamene adauzidwa kuti: “Khulupirirani mu zimene Mulungu wavumbulutsa”, iwo adati: “Ife 2:91 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:91) ayat 91 in Chichewa

2:91 Surah Al-Baqarah ayat 91 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 91 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَإِذَا قِيلَ لَهُمۡ ءَامِنُواْ بِمَآ أَنزَلَ ٱللَّهُ قَالُواْ نُؤۡمِنُ بِمَآ أُنزِلَ عَلَيۡنَا وَيَكۡفُرُونَ بِمَا وَرَآءَهُۥ وَهُوَ ٱلۡحَقُّ مُصَدِّقٗا لِّمَا مَعَهُمۡۗ قُلۡ فَلِمَ تَقۡتُلُونَ أَنۢبِيَآءَ ٱللَّهِ مِن قَبۡلُ إِن كُنتُم مُّؤۡمِنِينَ ﴾
[البَقَرَة: 91]

Ndipo pamene adauzidwa kuti: “Khulupirirani mu zimene Mulungu wavumbulutsa”, iwo adati: “Ife timakhulupirira m’mawu amene adavumbulutsidwa kwa ife.” Ndipo iwo sakhulupilira zimene zavumbulutsidwa posachedwapa ngakhale kuti ndicho choonadi, chimene chikutsimikiza zimene ali nazo. Nena: “Nanga ndi chifukwa chiyani inu mudali kupha Atumwi a Mulungu kale ngati, mudali okhulupiriradi?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا قيل لهم آمنوا بما أنـزل الله قالوا نؤمن بما أنـزل علينا, باللغة نيانجا

﴿وإذا قيل لهم آمنوا بما أنـزل الله قالوا نؤمن بما أنـزل علينا﴾ [البَقَرَة: 91]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akauzidwa (Ayuda): “Khulupirirani zimene Allah wavumbulutsa (kwa mtumiki Muhammad {s.a.w}).” Amanena: “Tikukhulupirira zimene zidavumbulitsidwa kwa ife,” ndipo amazikana zomwe sizili zimenezo ngakhale izo zili zoona, zomwe zikutsimikizira pa zimene ali nazo pamodzi. Nena: “Nanga bwanji mudapha aneneri a Allah kalelo ngati muli okhulupiriradi?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek